Genesis 1

1 PACIYAMBI Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi. 2 Dziko lapansi ndipo linali lopanda kanthu; ndipo mdima unali pamwamba pa nyanja; ndipo mzimu wa Mulungu unaliokufungatira pamwamba pa madzi. 3…

Genesis 2

1 Ndipo zinatha kupangidwa zakumwamba ndi dziko lapansi, ndi khamu lao lonse. 2 Tsiku lacisanu ndi ciwiri Mulungu anamariza nchito yonse anaipanga; ndipo anapuma tsiku lacisanu ndi ciwiri ku nchito…

Genesis 3

Kucimwa kwa Adamu ndi Hava 1 Ndipo njoka inali yakucenjera yoposa zamoyo zonse za m’thengo zimene anazipanga Yehova Mulungu, Ndipo inati kwa mkaziyo, Ea! kodi anatitu Mulungu, Usadye mitengo yonse…

Genesis 4

Kaini ndi Abele. Kuphedwa koyamba 1 Ndipo mwamunayo anadziwa mkazi wace Hava: ndipo anatenga pakati, nabala Kaini, ndipo anati, Ndalandira munthu kwa Yehova. 2 Ndipo anabalanso mphwace Abele. Abele anakhala…

Genesis 5

Mbumba ya Seti 1 Ili ndi buku la mibadwo ya Adamu. Tsiku lomwe Mulungu analenga munthu anamlenga m’cifanizo ca Mulungu; 2 anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi, nawadalitsa iwo nacha mtundu…

Genesis 6

Kulowerera kwa mtundu wa anthu 1 Ndipo panali pamene anthu anayamba kucuruka padziko, ndi ana akazi anawabadwira iwo, 2 kuti ana amuna a Mulungu anayang’ana ana akazi a anthu, kuti…

Genesis 7

Nowa ndi banja lace alowa m’cingalawa 1 Ndipo anati Yehova kwa Nowa, Talowani, iwe ndi a ku nyumba ako onse m’cingalawamo; cifukwa ndakuona iwe kuti uli wolungama pamaso panga m’mbadwo…

Genesis 8

Nowa aturuka m’cingalawa 1 Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m’cingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo pa dziko lapansi, naphwa madzi; 2 ndipo…

Genesis 9

Mulungu acita pangano ndi Nowa 1 Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ace, nati kwa iwo, Mubalane, mucuruke, mudzaze dziko lapansi. 2 Kuopsya kwanu, ndi kucititsa mantha kwanu kudzakhala pa…

Genesis 10

Mbumba ya Nowa 1 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu, ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana amuna, citapita cigumula cija. 2 Ana amuna a Yafeti: Gomeri,…